"Malawi Kwacha" has been designed by the Reserve Bank of Malawi to introduce the Kwacha banknotes in circulation and allows users to discover their security feature in an interactive way.
The app explains in an easy-to-follow way how to check the security features of a genuine Kwacha banknotes to distinguish it from counterfeit note. The security features are animated in an interactive way by tilting the phone or by using an integrated magnifier glass.
Main app features:
• Explore Banknotes: Learn about banknote security features and design, observe the banknote under UV light
• About the Reserve Bank of Malawi
• Available in: Chichewa and English
WARNING: This application does not verify the authenticity of the banknote, it only helps to identify and check security features.
Malawi kwacha ndi chipangizo chimene chakonzedwa ndi Banki yayikulu ya Malawi ndi cholinga chodziwitsa anthu za zizindikiro zodziwira ndalama yeniyeni ya Malawi kwacha munjira yamakono.
Chipangizochi chikulongosola mosavuta m’mene mungadziwire zizindikiro za ndalama yeniyeni kuti muthe kusiyanitsa ndi ndalama ya chinyengo. Zizindikiro zodziwira ndalamazi zayikidwa munjira yamakono ndipo mukhoza kupendeketsa foni yanu kapena kugwiritsa ntchito makina a padela okulitsa malembo amene akupezeka mkati mwa chipangizochi
Zazikulu za chipangizochi:
· Fufuzani za ndalama: phunzirani za zizindikiro za ndalama yanu ndi mapangidwe ake, komanso onetsetsetsani ndalamayi pa makina apadela( UV light)
· Zambiri ya Banki yayikulu ya Malawi
· Izi zikupezeka mu : Chichewa ndi chingerezi
CHENJEZO: chipangizochi sichingathe kutsimikizira kuti ndalama ndi yeniyeni kapena ayi, koma ndichothandiza kupeza ndi kudziwitsa zizindikiro zoti mudziwe pa ndalama yanu.